February 7-13
1 SAMUELI 1-2
Nyimbo 44 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Mukhuthulileni za Mumtima Mwanu Yehova M’pemphelo”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
1 Sam. 2:10—N’cifukwa ciani Hana anapemphela kuti Yehova “apeleke mphamvu kwa mfumu yake” pamene mu Isiraeli munalibe mfumu? (w05 3/15 21 ¶5)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, ni mfundo yopindulitsa iti imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) 1 Sam. 1:1-18 (th phunzilo 12)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Mukayamba na makambilano acitsanzo, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Yambani na makambilano acitsanzo. Kenako gaŵilani kabuku kakuti Kondwelani na Moyo Kwamuyaya!, na kukambilana mwacidule mbali yakuti “Zimene Muyenela Kucita Kuti Mupindule na Maphunzilo a Baibo Amenewa.” (th phunzilo 20)
Phunzilo la Baibo: (Mph. 5) lffi phunzilo 03 mfundo 5 (th phunzilo 13)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Acinyamata—Auzeni za Mumtima Mwanu Makolo Anu”: (Mph. 15) Kukambilana. Onetsani vidiyo yakuti Umoyo Wanga Nili Wacicepele—Kodi Ningakambe Nawo Bwanji Makolo Anga?
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lfb phunzilo 76
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 1 na Pemphelo