YEREMIYA 1-4
CUMA COPEZEKA M’MAU A MULUNGU |“Ine Ndili ndi Iwe Kuti Ndikulanditse”
Yeremiya ayenela kuti anali na zaka pafupi-fupi 25 pamene Yehova anamuika kukhala mneneli. Yeremiya anadziona kuti ni wosayenelela udindowo, koma Yehova anam’tsimikizila kuti adzapitiliza kum’thandiza.
-
647
Yeremiya aikidwa kukhala mneneli
-
607
Yerusalemu awonongedwa
-
580
Atsiliza kulemba
Madeti onse ni a mu B.C.E.