Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Maulaliki a Citsanzo

Maulaliki a Citsanzo

NSANJA YA MLONDA

Funso: M’kuona kwanu, muganiza mphatso yopambana zonse imene Mulungu anatipatsa ni iti?

Lemba: Yoh. 3:16

Cogaŵila: Magaziniyi ifotokoza cifukwa cake Mulungu anatuma Yesu kudzatifela, na mmene tingaonetsele kuyamikila mphatso imeneyo.

KODI UFUMU WA MULUNGU N’CIANI?

Funso: [Muonetseni kapepa kauthenga.] Mungayankhe bwanji funso iyi? Kodi ufumu wa Mulungu ni cinacake cimene cili mumtima mwanu? mau okuluŵika? kapena boma lakumwamba?

Lemba: Dan. 2:44; Yes. 9:6

Cogaŵila: Kapepa aka kaonetsa mmene Ufumu wa Mulungu ungakupindulitsileni.

CIITANO CA KU CIKUMBUTSO

Kugaŵila Kapepa ka Ciitano: Tiitanila anthu ku cocitika cofunika kwambili. [Mpatseni ciitano.] Pa 11 April, anthu mamiliyoni padziko lonse adzasonkhana kuti akumbukile imfa ya Yesu, na kumvetsela nkhani ya Baibo kwaulele. Nkhaniyo idzaonetsa mmene tingapindulile na imfa ya Yesu. Kapepa ka ciitano aka kaonetsa nthawi na malo kumene kudzacitikila mwambo umenewu kuno kwathu. Tidzakondwela ngati mungabwele.

KONZANI ULALIKI WANU

Funso:

Lemba:

Cogaŵila: