CITANI KHAMA PA ULALIKI
Makambilano Acitsanzo
Ulendo Woyamba mu November (Kampeni Yapadela)
Funso: Kodi n’zoona kuti nkhondo komanso zaciwawa zidzatha?
Lemba: Sal. 37:10, 11
Ulalo: Ni lonjezo liti la m’Baibo limene limatipatsa ciyembekezo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:
Ulendo Woyamba mu December *
Funso: Kodi Baibo mumaiona bwanji?
Lemba: Aroma 15:4
Ulalo: Ni lonjezo liti la m’Baibo limene limatipatsa ciyembekezo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:
Ulendo Wobwelelako *
Funso: Ni lonjezo liti la m’Baibo limene limatipatsa ciyembekezo?
Lemba: Chiv. 21:3, 4
Ulalo: Kodi n’ciani cingatithandize kuimvetsetsa Baibo?
PEZANI LEMBALI M’CIDA CA M’THUBOKSI YATHU:
^ ndime 9 ^ ndime 15 Mungasintheko funso na ulalo kuti zigwilizane na mikhalidwe ya kwanuko.