CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
Cikondi ca Mulungu Cosasintha Cimatiteteza ku Mabodza a Satana
Satana amafuna kuti anthu azikhulupilila kuti Yehova ndiye amacititsa zinthu zoipa (Yobu 8:4)
Iye amafuna tiziganiza kuti Yehova alibe nazo kanthu zakuti kaya ndife okhulupilika kwa iye kapena ayi (Yobu 9:20-22; w15 7/1 12 ¶3)
Cikondi ca Yehova cosasintha cimatiteteza kuti tisasoceletsedwe na mabodza a Satana komanso kuti tikhalebe okhulupilika (Yobu 10:12; Sal. 32:7, 10; w21.11 6 ¶14)
YESANI KUCITA IZI: Kuti mukhalebe wolimba pokumana na mayeso, ganizilani mmene Yehova akuonetsela cikondi cake cosasintha kwa inu. Kenako lembani zimene mwapeza na kumaziŵelenga kaŵili-kaŵili.