September 18-24
ESITERE 6-8
Nyimbo 115 na Pemphelo
Mawu Oyamba (Mph. 1)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Citsanzo Cimene Tingatengele pa Nkhani ya Kulankhulana Bwino”: (Mph. 10)
Kufufuza Cuma Cauzimu: (Mph. 10)
Esitere 7:4—Kodi kuwonongedwa kwa Ayuda ‘kukanawonongetsa bwanji zinthu zambili za Mfumu’? (w06 3/1 11 ¶1)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno ni mfundo iti yokupindulilani imene munapeza yokhudza Yehova, ulaliki, kapena mfundo ina iliyonse?
Kuŵelenga Baibo: (Mph. 4) Esitere 8:9-17 (th phunzilo 5)
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (Mph. 3) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Mukayamba, mwininyumba akambe mawu ofala kwanuko ofuna kukanila ulaliki, koma mwaluso loŵelani pa mawu amenewo. (th phunzilo 3)
Ulendo Wobwelelako: (Mph. 4) Makambilano anu atsamile pa mfundo yaikulu ya makambilano acitsanzo. Muitanileni ku misonkhano. Kenako, chulani na kukambilanako vidiyo yakuti N’ciani Cimacitika ku Nyumba ya Ufumu? (Koma musaitambitse.) (th phunzilo 12)
Nkhani: (Mph. 5) w22.01 10-11 ¶8-10—Mutu: Muziphunzitsa Mogwila Mtima Monga Yakobo—Uthenga Wanu Uzikhala Wosavuta Kumva. (th phunzilo 17)
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Muzidalila Yehova Pamene Mukuvutitsidwa”: (Mph. 15) Kukambilana na kutamba vidiyo.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (Mph. 30) lff phunzilo 58
Mawu Othela (Mph. 3)
Nyimbo 124 na Pemphelo