October 21-27
MASALIMO 100-102
Nyimbo 37 na Pemphelo | Mawu Oyamba (Mph. 1)
1. Onetsani Kuti Mumayamikila Cikondi Cosasintha ca Yehova
(Mph. 10)
Kulitsani cikondi canu pa Yehova (Sal. 100:5; w23.03 12 ¶18-19)
Pewani zinthu zimene zingawononge ubale wanu na Yehova (Sal. 101:2, 3; w23.02 17 ¶10)
Pewani anthu amene amaipitsa dzina la Yehova na gulu lake (Sal. 101:5; w11-CN 7/15 16 ¶7-8)
DZIFUNSENI KUTI, ‘Kodi zina zimene nimacita poseŵenzetsa soshomidiya zingawononge ubale wanga na Yehova?’
2. Kufufuza Cuma Cauzimu
(Mph. 10)
Sal. 102:6—N’cifukwa ciyani wamasalimo anadziyelekezela na mbalame yochedwa vuwo? (it-2-E 596)
Pa kuŵelenga Baibo kwa mlungu uno, munapeza mfundo zothandiza ziti zimene mungakonde kutifotokozelako?
3. Kuŵelenga Baibo
(Mph. 4) Sal. 102:1-28 (th phunzilo 12)
4. Kuyambitsa Makambilano
(Mph. 3) KUNYUMBA NA NYUMBA. (lmd phunzilo 2 mfundo 3)
5. Kubwelelako
(Mph. 5) KUNYUMBA NA NYUMBA. M’pempheni kuti muyambe kuphunzila naye Baibo. (lmd phunzilo 9 mfundo 4)
6. Kufotokoza Zimene Mumakhulupilila
(Mph. 4) Citsanzo. ijwbq 129—Mutu: Kodi Baibo Anaisintha Kapena Anangoisinthako Zina? (th phunzilo 8)
Nyimbo 137
7. ‘Nakulondolani Kulikonse; Ndipo Inu Mwanigwila mwa Mphamvu’
(Mph. 15)
Kukambilana. Tambitsani VIDIYO. Kenako funsani omvela kuti:
Kodi Anna anaonetsa bwanji cikondi cosasintha?
Nanga tingatengele bwanji citsanzo cake?
8. Phunzilo la Baibo la Mpingo
(Mph. 30) bt mutu 17 ¶1-7