4-E
Zocitika zazikulu za paumoyo wa Yesu Padziko—Utumiki wa Yesu ku Galileya (Mbali 3) ku Yudeya
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, pambuyo pa Pasika |
Nyanja ya Galileya; Betsaida |
M’bwato paulendo wa ku Betsaida, Yesu acenjeza za cofufumitsa ca Afalisi; acilitsa munthu wakhungu |
||||
Dela la Kaisara wa ku Filipi |
Makiyi a Ufumu; anenelatu za imfa ndi kuukitsidwa kwake |
9:18-27 |
||||
Mwina Phili la Herimoni |
Kusandulika; Yehova alankhula |
9:28-36 |
||||
Cigawo ca Kaisareya wa Filipi |
Acilitsa mnyamata wakhunyu |
9:37-43 |
||||
Galileya |
Anenelatunso za imfa yake |
9:43-45 |
||||
Kaperenao |
Akhoma msonkho ndi kobidi ya mkamwa mwa nsomba |
|||||
Wamkulu mu Ufumu; mafanizo a nkhosa yotaika ndi kapolo wosakhululukila |
9:46-50 |
|||||
Galileya-Samariya |
Ulendo wa ku Yerusalemu, auza ophunzila ake kuti adzafunika kuika Ufumu poyamba |
9:51-62 |
7:2-10 |
Utumiki wa Yesu Wakumapeto mu Yudeya
NTHAWI |
MALO |
COCITIKA |
MATEYU |
MALIKO |
LUKA |
YOHANE |
---|---|---|---|---|---|---|
32, Cikondwelelo ca Misasa |
Yerusalemu |
Aphunzitsa pa Cikondwelelo ca Misasa; asilikali abwela kudzamugwila |
7:11-52 |
|||
Anena kuti “Ine ndine kuwala kwa dziko”; acilitsa munthu wakhungu |
8:12–9:41 |
|||||
Mwina ku Yudeya |
Atumiza atumwi 70; abwelako osangalala |
10:1-24 |
||||
Yudeya; Betaniya |
Fanizo la Msamariya wacifundo; Apita kukaceza kunyumba ya Mariya ndi Marita |
10:25-42 |
||||
Mwina ku Yudeya |
Aphunzitsanso pemphelo la citsanzo; fanizo la bwenzi loumilila |
11:1-13 |
||||
Kutulutsa ziŵanda ndi cala ca Mulungu; apelekanso cizindikilo ca Yona |
11:14-36 |
|||||
Akudya ndi Mfalisi; atsutsa cinyengo ca Afalisi |
11:37-54 |
|||||
Mafanizo: munthu wacuma wopanda nzelu ndi mtumiki wokhulupilika |
12:1-59 |
|||||
Acilitsa mai wopunduka pa Sabata; mafanizo a kanjele ka mpilu ndi zofufumitsa |
13:1-21 |
|||||
32, Cikondwelelo Copeleka Kacisi |
Yerusalemu |
Mafanizo a m’busa wabwino ndi khola la nkhosa; Ayuda ayesa kumponya miyala; apita ku Betaniya kutsidya la Yorodano |
10:1-39 |