16-A
Mlungu Womaliza wa Moyo wa Yesu Padziko Lapansi (Mbali 1)
Nisani 8 (Sabata)
KULOŴA KWA DZUŴA Masiku Aciyuda anali kuyamba ndi kutha poloŵa dzuŵa
-
Afika ku Betaniya masiku 6 Pasika asanacitike
-
Yohane 11:55–12:1
KUTULUKA KWA DZUŴA
KULOŴA KWA DZUŴA
Nisani 9
KULOŴA KWA DZUŴA
-
Akudya ndi Simoni wakhate
-
Mariya adzoza Yesu ndi nado
-
Ayuda abwela kudzaona Yesu ndi Lazaro
-
Yohane 12:2-11
KUTULUKA KWA DZUŴA
-
Aloŵa m’Yerusalemu monga mfumu
-
Aphunzitsa m’kacisi
-
Luka 19:29-44
-
Yohane 12:12-19
KULOŴA KWA DZUŴA]
Nisani 10
KULOŴA KWA DZUŴA]
-
Agona ku Betaniya
KUTULUKA KWA DZUŴA
-
Alaŵilila ku Yerusalemu
-
Ayeletsa kacisi
-
Yehova alankhula kucokela kumwamba
-
Luka 19:45-48
-
Yohane 12:20-50
KULOŴA KWA DZUŴA
Nisani 11
KULOŴA KWA DZUŴA
KUTULUKA KWA DZUŴA
-
Aphunzitsa m’kacisi, pogwilitsila nchito mafanizo
-
Adzudzula Afalisi
-
Aona copeleka ca mkazi wa masiye
-
Paphili la Maolivi, anenelatu mmene Yerusalemu adzagwela ndi kupeleka zizindikilo za kukhalapo kwake mtsogolo
-
Luka 20:1–21:38
KULOŴA KWA DZUŴA