Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa mu 2020

Pulogilamu ya Msonkhano Wacigawo wa Mboni za Yehova wa mu 2020, wa mutu wakuti ‘Kondwelani Nthawi Zonse’!

Tsiku Loyamba

Pulogilamu ya tsiku loyamba yazikidwa pa Afilipi 4:4—‘Kondwelani nthawi zonse mwa Ambuye. Ndibwelezanso, Kondwelani’!

Tsiku Laciŵili

Pulogilamu ya tsiku laciŵili yazikidwa pa Salimo 105:3—“Nyadilani dzina lake loyela. Mtima wa anthu ofunafuna Yehova usangalale.”

Tsiku Lacitatu

Pulogilamu ya tsiku lacitatu yazikidwa pa Salimo 37:4—“Sangalala mwa Yehova, ndipo adzakupatsa zokhumba za mtima wako.”

Mawu kwa Osonkhana

Mawu othandiza kwa opezeka pa msonkhano wacigawo