Thandizo Ilipo
Kodi munthu amene mumam’konda anamwalila?
Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “Thandizo Kwa Ofedwa.”
Kodi mumakumana na mavuto azacuma?
Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “moseŵenzetsela ndalama.”
Kodi munadzifunsapo kuti, ‘Kodi kukhala na moyo kuli na phindu kwa ine?’
Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “mukafika pakuti simufunanso kukhala na moyo” komanso akuti “kodi moyo ukali na phindu kwa ine?”
Kodi mulimbana na matenda osacilitsika?
Yendani pa jw.org, na kufufuza mawu akuti “munthu amene mukonda akadwala matenda osacilitsika.”
Baibo imapeleka malangizo opindulitsa kwambili kwa aliyense m’banja. Ndipo mfundo zake zimathandiza munthu kukhala woganiza bwino, komanso kupanga zosankha zanzelu.—MIYAMBO 1:1-4.
Tikupemphani kuti mudziŵelengele mwekha Baibo. Tambani vidiyo yakuti, N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo?.