Mungakhale pa Ubwenzi na Mulungu
ANTHU ENA AMAONA KUTI . . .
Mulungu sasamala za ise ndipo ni wapamwamba kwambili, woyela, komanso wosafikilika.
ZIMENE BAIBO IMAKAMBA
“Yandikilani Mulungu, ndipo iyenso adzakuyandikilani.”—Yakobo 4:8.
‘M’tulileni nkhawa zanu zonse, pakuti amakudelani nkhawa.’—1 Petulo 5:7.
KODI TINGACITE CIANI KUTI TIKHALE PA UBWENZI NA MULUNGU?
Muzikamba naye.—Salimo 145:18, 19.
Muzimumvela.—Salimo 32:8.
Muzitsatila malangizo ake.—Miyambo 3:5, 6.
Limbikilani kuti mukhale bwenzi lake.—Mateyu 7:7, 8.