Mau Oyamba
MUGANIZA BWANJI?
Kodi mungapindule ndi mau odziŵika bwino akuti:
“Mulungu anakonda kwambili dziko mwakuti anapeleka Mwana wake wobadwa yekha”? —Yohane 3:16.
Nsanja ya Mlonda iyi, ifotokoza mmene mungapindulile cifukwa cakuti Yesu anavutika ndi kutifela.