NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA May 2016

M’magazini ino muli nkhani zophunzila milungu ya June 27 mpaka July 31, 2016.

Tizithetsa Mikangano Mwamtendele

Kodi colinga canu ciyenela kukhala ciani? Kuwina mkangano, kucititsa munthu kuvomeleza kuti ndi wolakwa, kapena ciani?

“Pitani Mukaphunzitse Anthu a Mitundu Yonse Kuti Akhale Ophunzila”

Mayankho a mafunso anai atithandiza kudziŵa anthu amene akukwanilitsa ulosi wa Yesu masiku ano.

Kodi Mumasankha Bwanji Zocita?

Kodi muyenela kucita ciani ngati mufuna kupanga cosankha pa nkhani imene m’Baibulo mulibe lamulo lacindunji?

Kodi Baibulo Likusinthabe Umoyo Wanu?

Munthu wina wa Mboni za Yehova analeka kuchova njuga, kukoka fodya, kumwa mwaucidakwa, ndi kugwilitsila nchito mankhwala osokoneza bongo kuti ayenelele ubatizo, koma anaona kuti cinthu cina cinali covuta kwambili kusintha.

Pindulani Mokwanila ndi Cakudya Cakuuzimu Cimene Yehova Amapeleka

Kodi ndi maganizo otani amene angatilepheletse kupindula mokwanila ndi cakudya cakuuzimu cimene timalandila?