NSANJA YA MLONDA—YOPHUNZILA November 2014
Magazini ino ili ndi nkhani zophunzila za December 29, 2014 mpaka February 1, 2015.
Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu Kumatanthauza Ciani kwa Ife?
Pali mfundo zinai zimene zimapeleka umboni wosatsutsika wakuti Yesu anaukitsidwadi. Kukhulupilila kuti Yesu anauka kuyenela kutikhudza bwanji?
Cifukwa Cake Tifunika Kukhala Oyela
Kodi mfundo za m’buku la m’Baibulo la Levitiko zimakuvutani kumvetsetsa kapena zimakucititsani ulesi? Mfundo zamtengo wapatali zopezeka m’buku la Levitiko, zingakuthandizeni kulambila Mulungu m’njila yovomelezeka.
Tifunika Kukhala Oyela m’Makhalidwe Athu Onse
Kodi kupewa kupeputsa malamulo, kupatsa Yehova zabwino koposa, ndi kudya cakudya cotafuna ca kuuzimu zifanana bwanji?
“Anthu Amene Mulungu Wao Ndi Yehova”
Kodi Mulungu amayanja anthu onse amene amam’lambila, mosasamala kanthu za cipembedzo cao?
‘Tsopano Ndinu Anthu a Mulungu’
Kodi tingakhale motani “anthu a Mulungu” ndi kupitilizabe kutelo?
Mafunso Ocokela kwa Aŵelengi
Kodi akulu ndi atumiki othandiza amaikidwa bwanji pa udindo mumpingo? Kodi mboni ziŵili zochulidwa pa Chivumbulutso caputala 11 ndani?
ZA M'NKHOKWE YATHU
Kuwala kwa Coonadi Kufika m’Dziko la Japan
Magalimoto ochedwa “Yehu” anathandiza kuti nchito yolalikila za Ufumu ku Japan ipite patsogolo.