Mlozela Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Mlonda a 2014
Tasonyeza deti la magazini imene muli nkhani
BAIBULO
Linalembedwa Bwanji? 2/1
Ndi Maudi a Mulungu? 2/1
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Kulikonse kumene ndinali kupita, ndinali kukhala ndi mfuti yanga (A. Lugarà), 7/1
Ndinali wodzikonda (C. Bauer),—November-December
Ndinamenya nkhondo yandekha kuti ndithetse kupanda cilungamo ndi nkhanza (A. Touma),—September-October
MAFUNSO OCOKELA KWA AŴELENGI
MBILI YANGA
MBONI ZA YEHOVA
NKHANI ZOPHUNZILA
Khalani ndi Mzimu Wodzimana, 3/1
Kodi Kuukitsidwa kwa Yesu Kumatanthauza Ciani kwa Ife? 11/15
Kodi Mumakhulupilila Kuti Muli ndi Coonadi? N’cifukwa Ciani? 9/15
Kodi Mumaona “Wosaonekayo”? 4/1
Kodi Mumaona Zofooka za Anthu Mmene Yehova Amazionela? 6/1
Kodi Mumayamikila Cisamalilo Cacikondi ca Yehova? 4/1
Kodi Mumayendela Limodzi ndi Gulu la Yehova? 5/1
Kodi Ulamulilo wa Yesu wa Zaka 100 Wakupindulitsani Bwanji? 1/1
Limbani Mtima Yehova ndi Mthandizi Wanu, 4/1
Mmene Tingakhalilebe ndi Maganizo Oyenela, 3/1
Mmene ‘Tingayankhile Munthu Wina Aliyense’, 5/1
Muzilemekeza Okalamba Ali Pakati Panu, 3/1
Muzionetsa Khalidwe Lopambana mu Ulaliki, 5/1
Muzisamalila Okalamba, 3/1
Palibe Munthu Angatumikile Ambuye Aŵili, 4/1
Sangalalani Cifukwa ca Cikwati ca Mwanawankhosa, 2/1
Tamandani Kristu, Mfumu Yaulemelelo, 2/1
Thandizani Ena Kupita Patsogolo, 6/1
Tikhale Ogwilizana Pamene Mapeto a Dzikoli Ayandikila, 12/15
Tsanzilani Cikhulupililo ca Mose, 4/1
Tumikilani Mulungu Mokhulupilika Panthawi ya “Masautso Ambili,” 9/15
“Uzikonda Mnzako Mmene Umadzikondela Wekha,” 6/1
“Uzikonda Yehova Mulungu Wako,” 6/15
Yehova Amatisamalila ndi Kutiteteza, 2/1
Yehova Ndi Bwenzi Lathu Lapamtima, 2/1
Yehova ndi Mulungu wa Dongosolo, 5/1
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Anapilila Zinthu Zopanda Cilungamo, (Eliya), 2/1
Cipembedzo Coona,—September-October
Colinga ca Dziko Lapansi, 6/1
Gulaye pomenya nkhondo m’nthawi zakale, 5/1
Kodi Anthu Adzaononga Dziko Lapansi Kothelatu?—November-December
Kodi Cilamulo ca Mulungu kwa Aisiraeli Cinali Colungama ndi Cosakondela?—November-December
Kodi oyenda panyanja akalekale anali kupanga bwanji ngalawa zao kuti madzi asaziloŵa?—July-August
Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulila?—November-December 11/1
Mgwilizano wa Zipembedzo, 3/1
Mkate Wamoyo, 6/1
Mmene Mungalangile Ana Anu—July-August
Mulungu Amakuona Bwanji Kukoka Fodya? 6/1
N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela Kuti Ufumu Ubwele?—November-December
N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela? Tizipemphela Bwanji?—July-August
N’cifukwa Ciani Zigaŵenga Anali Kuzithyola Miyendo Pozipha? 5/1
N’cifukwa Ciani Zoipa Zimacitikila Anthu Abwino?—July-August
Ndani Amadziŵa Zamtsogolo? 5/1
Ndani Kwenikweni Akulamulila Dzikoli? 5/1
Nkhondo Imene Inasintha Zinthu Padziko (Nkhondo yoyamba ya padziko lonse), 2/1
Pali Ciyembekezo Cotani Ponena za Makolo Akale? 6/1
‘Tamvelani Maloto Awa’ (Yosefe),—September-October
UMOYO NDI MAKHALIDWE ACIKRISTU
Kulambila Kwa Pabanja, 3/1
N’cifukwa Ciani Tiyenela Kupemphela? 4/1
YEHOVA
Kodi Amacita Nanu Cidwi?—September-October
Mulungu Wosaonekayo Mungamuone?—July-August
Ndani Anapanga Mulungu?—September-October
Zimene Mulungu Wakucitilani, 3/1
YESU KRISTU
Adzacita ciani mtsogolo? 4/1
Akucita ciani tsopano? 4/1
Cocitika Cimene Simuyenela Kuphonya (Cikumbutso), 3/1
Timapindula bwanji ndi imfa ya Yesu? 3/1
Tiyenela kukumbukila bwanji imfa ya Yesu? 3/1