Nyimbo Zopekedwa Koyamba
Nyimbo zathu zoonetsa ciyamikilo pa colowa cathu cauzimu.
Sitidzakuiŵalani
Sitimaiŵalidwa pa nthawi ya mavuto.
“Lemekezani Yehova na Cuma Canu”
Tingamupatse ciani Yehova kuti timusangalatse mtima?
N’dzakutumikilani na Moyo Wanga Wonse
Patsani Mulungu zabwino koposa pamene mukali acicepele.
Kungomwetulila
Kumwetulila kungathandize mu ulaliki na mu umoyo wathu.
Cimwemwe ca Misonkhano Ikulu
Tikapezeka pa msonkhano wacigawo, timaona mgwilizano na cikondi ca abale padziko lonse.
Nakupatsani Mphatso Yabwino Koposa
Si cinthu copepuka makolo kuona mwana wawo apita kumalo akutali.
Yembekeza, Usankhe Bwino
Ngati tifunafuna munthu womanga naye banja, tifunika kudekha na kusankha mwanzelu.
Ganizila Moyo Wam’tsogolo
Tikuyembekezela tsiku latsopano kutsogoloku.
Tithamange, Tisatsalile
Tithamange pamodzi na gulu la Yehova!
Uzidekha
Timacita bwino mu utumiki komanso m’mbali zina za umoyo wathu ngati sitithamangila ndiponso ticita zinthu modekha.
“Tikhale Oceleza Alendo”
Ni m’njila ziti za mmene tingacelezele ena?
Tiyamikila
Kupitila mwa mzimu wake, Yehova amatithandiza kupilila mavuto aliwonse amene tingakumane nawo. Cifukwa cokhudzika, tikuimba nyimbo iyi yomuyamikila.
Kucita Zoyenela
Kodi mungaimupeze bwanji bwenzi labwino koposa?
Tizikhululukilana
Sakilani mipata mu umoyo wanu kuti mutengele citsanzo ca Yehova na kukhululukila ena.
Dziko Latsopano Ili Pafupi Kwambili
Kuyembekezela paradaiso kusogoloku kungatithandize kupilila.
Mawu Anu ni Osatha
Tamandani Mulungu cifukwa coteteza Mawu ake kaamba ka anthu!
Dekhani ndipo Pemphelani
Tikakumana na mavuto, kodi tingacite ciani?
Kumanga Tsogolo Langa na Yehova
Muzikondweletsa Yehova tsiku lililonse na zosankha zimene mumapanga.
Cikhulupililo Cingapangitse Kucita Zinthu Zazikulu
Kulimbitsa cikhulupililo cathu kumafuna khama, koma Yehova adzatidalitsa pa khama limenelo.
Nimasunga Zikumbutso Zanu
Mwa mawu athu na zocita zathu, tiyeni tionetse kuti timakondadi zikumbutso za Yehova.
Ninganyamuke
Limbikitsani mtumiki wokangalika wa Yehova amene anazilala pamene akuyesa kupeza mphamvu zakuti abwelele mu mpingo wacikondi.
Timadabwa Na Nchito Zanu
Muziyamikila mwayi wanu woseŵenza na Yehova!
Mwana Wamkazi Wokondedwa
Tate akuona mwana wake pamene akula m’kupita kwa zaka komanso pamene apanga coonadi kukhala cake cake.
Tiyenibe
Kuwonjezela utumiki wathu mwa njila iliyonse kungatithandize ise atumiki a Yehova kupeza cimwemwe.
Mvetsela na Kuona
Seŵenzetsani bwino nthawi imene muli nayo yoceza na abale komanso alongo anu.
Nchito Zanu Zodabwitsa Zimanilimbikitsa
Nchito za manja a Yehova zimatidabwitsa ndipo zitilimbikitsa kuti timuimbile.
Zinthu Zofunika
Tifunika kupatula nthawi yocita zinthu zofunika monga kupemphela, kuŵelenga, na kudzipeleka kwa Mulungu.
Tikondanadi
Kukhala na Yehova Mulungu mu cikwati canu kudzalimbitsa banja lanu!
Malo Amene Adzakubweletselani Citamando
Ndise okondwela kupeleka malo amene adzacititsa kuti dzina lake litamandidwe.
Kudalila Imwe
Kuŵelenga na kusinkhasinkha mawu a Mulungu kungatithandize kupilila mavuto amene ali monga cimphepo camkuntho mu umoyo.
Nidzasinthadi
Kodi mwalimbikitsidwa kuti mupange masinthidwe pa utumiki wanu?
Sitili Tekha
Ngati tili kumbali ya Yehova ndiye kuti sitili tekha!
Cikondi ca Paubale
Anthu a Yehova m’dzikoli amathandizana kuposa mmene ena onse.
Musayope
Tikakumana na mavuto mu umoyo, tizikumbuka kuti sitili tekha.
Kufuna-funa
Anthu amene moona mtima amafuna kudziŵa Mulungu amayesetsa kumufuna-funa.
Mabwenzi Azoona
Kodi mabwenzi azoona tingawapeze kuti?
Unganidalile
Pa nthawi yabwino komanso yovuta, tingadalile mabwenzi athu eni-eni.
Kwa Yehova, Ndise Amodzi
Ngakhale kuti tikukhala m’dziko loipa, timakhala mwamtendele komanso ogwilizana m’gulu lathu la abale.
Nilimbitseni Mtima
Yehova tilimbitseni mitima kuti tikwanitse kupilila mayeselo amene tingakumane nawo.
Nikupatsani Zonse Nili Nazo
Yehova ni woyeneladi kum’tumikila na moyo wathu wonse.
Tsiku Iliyonse ili na Nkhawa Zake
Tingapeze mtendele na cimwemwe ngakhale kuti tili na mavuto
Limba, Khala na Mphamvu
Nyimbo yapadela imene imatithandiza kupilila.
Nimayamikila Cilengedwe ca Mulungu
Pezani nthawi yosinkha-sinkha za cilengedwe ca Yehova ndiyeno muyamikileni m’pemphelo.
Ndise Banja Lanu
Kulikonse kumene tingakhale, ndise a m’banja la Yehova.
“Menya Nkhondo Yabwino Ya Cikhulupililo”
Olo tikumane na mavuto na zolimbana nazo, tingakhalebe wokhulupilika kwa Yehova.
Yehova Ali Na Ise Nthawi Zonse
Yehova ni wofunitsitsa kukuthandiza.
Dziko Latsopano Likubwelalo
Zimene timaona m’maganizo mwathu zimakhudza kalingalilidwe kathu. Nyimbo iyi itithandiza kuganizila za dziko latsopano.
Nikupatsani Moyo Wanga
Cifukwa ca cikondi cathu pa Yehova, timapita patsogolo mpaka kudzipatulila na kubatizika.
M’tulile Nkhawa Zako
Ngati ndimwe wopsinjika maganizo, pitilizani kudalila Yehova kuti akupatseni mphamvu na kukutonthozani.
Tikhale Monga Mwana
Kodi tingakhale bwanji monga mwana poonetsa ena cikondi?
M’sakaikile
Tingakhale opanda cikaiko cakuti Yehova amatikonda mosasamala kanthu za mayeselo amene tikumana nawo.
Khululuka na Mtima Wonse
Kodi munthu wina anakukhumudwitsani? Kodi n’zovuta kwa inu kuti mum’khululukile? Onani mmene mungam’khululukile na Mtima Wonse.
Tithamange pa Mpikisano
Pangani zosankha zanzelu kuti mupambane mpikisano wokapeza moyo.
“Kondwelani Nthawi Zonse”
Nyimbo ya cisangalalo imatikumbutsa kuti tili na zifukwa zambili zokhalila okondwela.
Cimwemwe Cathu Camuyaya
Yehova ndiye gwelo leni-leni la cimwemwe cathu ku nthawi zonse.
M’patulileni Nthawi Yehova
Kukhala wotangwanika potumikila Yehova ndiye umoyo wabwino koposa.
Mwa Cikhulupililo
Ganizilani za tsogolo locititsa kaso limene Mulungu wasungila anthu.
Banja la Yehova
Pali anthu ambili m’dzikoli amene akali kufuna-funa coonadi. Vidiyo iyi idzakulimbikitsani kufuna-funa anthu onga nkhosa.
Pamodzi Tilimba
Tingakwanitse kupilila mavuto alionse cifukwa ca thandizo la banja lathu logwilizana la padziko lonse komanso thandizo la Yehova.
Ningapitenso Kwa Ndani?
Tumikilani mokhulupilika kwa moyo wanu wonse monga mtumiki womvela mawu a m’busa wake.
Nidziŵa Yehova Ali Nane
Na thandizo la Yehova, tingagonjetse mantha aliwonse.
Ukagwa, Phunzilapo
Ngati waphunzilapo pa zimene unalakwitsa, udzakhala wolimba kuposa kale.
Funa Moyo Wamuyaya
Tingakhale na moyo wacimwemwe komanso watanthauzo lomba komanso m’tsogolo.
Mtendele Wosatha Pamapeto Pake! (2022 Nyimbo ya Pamsonkhano Wacigawo)
Yang’anani pa lonjezo la Mulungu la mtendele weniweni, osati pa mavuto amene mukumana nawo.
Uniyandikile
Mulungu amacita cidwi kwambili na onse amene amafuna kumuyandikila mosasamala kanthu za kumene akhala.
“Silidzacedwa!” (Nyimbo ya pa Msonkhano Wacigawo wa 2023)
Tengelani citsanzo ca anthu okhulupilika poyembekezela Yehova moleza mtima.
Atidziŵa Bwino
Yehova amatidziŵa bwino aliyense wa ife ndipo amamvetsa mmene timamvela mumtima.
Capamodzi Tidzamuimbila Mokondwa Yehova
Timakondwela na mtendele umene umabwela cifukwa cotumikila Yehova.
Tisaleke Kulalikila
Dalilani Yehova, ndipo lalikilani olo kuti muli na mantha.
“Uthenga Wabwino”! (Nyimbo ya pa Msonkhano Wacigawo wa 2024)
Kuyambila m’zaka za zana loyamba mpaka masiku ano, mwacimwemwe anthu akhala akulalikila uthenga wabwino. Uthengawo ni wofunika kwambili kuposa uthenga wina ulionse cifukwa umakamba za nchito imene Yesu iye mwini anaiyambitsa, komanso mmene angelo amamuthandizila pa nchitoyi.
Ima, Uone Zinthu Mwatsopano
Kodi kusinkhasinkha cilengedwe ca Mulungu kungatithandize bwanji kuona zinthu mwatsopano ndi kukwanitsa kulimbana ndi mavuto pa moyo wathu?
Tifune Zocepa
Tidzakhaladi acimwemwe ngati timakhutila ndi zinthu zocepa zomwe Yehova amatipatsa.
Kukhala Mwamtendele M’dziko Lopanda Mtendele
Kukhala mwamtendele kumalemekezetsa Yehova.
Mphamvu Yoposa Yanga
Onani kuti “anthu amene alibe wowathandiza, Mulungu amawapatsa nyumba kuti azikhalamo.”
M’patseni Ulemelelo Yehova
Kukonda Yehova komanso kumuyamikila kumacititsa kuti timupatse ulemelelo.