Kukhala Mwamtendele M’dziko Lopanda Mtendele
Citani Daunilodi:
1. Kulikonse ningayang’ane niona anthu oopsa.
Anthu ambili amavutika tsiku na tsiku.
Koma Yehova amafuna tikhale acifundo
Komanso kuti tizipemphela kwa iye nthawi zonse.
(KOLASI)
Ngati ndife anthu a mtendele m’dziko lino lovuta,
Sitidzavutikanso kucita zinthu mwamtendele m’paradaiso!
2. Nako kunchito mikangano imabuka wambawamba.
Mikangano ni yoipa, imathetsa mtendele.
Ine nimakumbuka Mawu a Mulungu nthawi zonse
Ndipo nimafuna kuonetsa cifundo kwa anthu onse.
(KOLASI)
Ngati ndife anthu a mtendele m’dziko lino lovuta,
Sitidzavutikanso kucita zinthu mwamtendele m’paradaiso!
(BILIJI)
Inde sicopepuka
Kupitiliza kusunga
Mtendele m’dziko lovutali,
Koma tidalile M’lungu.
3. Pamene tili mu ulaliki timapezanso anthu
Omwe amatikwiyila kwambili tikawalalikila.
Koma timasunga mtendele mwa kucoka panyumbayo.
Timawasiya kuti tisunge mtendele nthawi zonse.