Onani zimene zilipo

Onani nkhani zake

Ningapitenso Kwa Ndani?

Ningapitenso Kwa Ndani?

Daunilodi:

  1. 1. M’nthawi ino yovuta

    Nimamvela Yesu.

    Nimatsatila

    Malangizo ake.

    Ni M’busa Wabwino,

    Mpulumutsi wanga.

    Nimam’dalila,

    Sanganisoceze.

    (MWANA WA KOLASI)

    Ine sin’dzamvetsela

    kwa otsutsa coonadi,

    Ine sin’dzalola

    Kuti anisoceze.

    (KOLASI)

    N’ngapitenso kwa ndani?

    Nikakhala pa mavuto

    Ningapitenso kwa ndani?

    Ine sin’dzamvela

    Mawu acilendo.

    Nidzamvela Yesu kosatha.

  2. 2. Ndine wotetezeka,

    Ndine wokhutila,

    Ndine wokondwa,

    M’gulu lacikondi.

    Niyembekezela tsogolo lowala

    Limene Yehova wanilonjeza.

    (MWANA WA KOLASI)

    Sinidzamvetsela

    kwa otsutsa coonadi

    Ine sin’dzalola

    Kuti anisoceze.

    (KOLASI)

    N’ngapitenso kwa ndani?

    Nikakhala pa mavuto

    Ningapitenso kwa ndani?

    Ine sin’dzamvela

    Mawu acilendo.

    Nidzamvela Yesu kosatha.

    (KOLASI)

    N’ngapitenso kwa ndani?

    Nikakhala pa mavuto

    Ningapitenso kwa ndani?

    Ine sin’dzamvela

    Mawu acilendo.

    Nidzamvela Yesu kosatha.

    N’ngapitenso kwa ndani?

    Kulibe kwina ningapite.