Uniyandikile
Daunilodi:
1. Sin’ngaiŵale,
N’nalidi munthu wotayika ndithu.
Ndipo n’nali na mantha.
M’lungu ananithandiza.
Iye amanitonthoza,
Amaniuza kuti:
(KOLASI)
“Uniyandikile, inenso
N’dzakuyandikila.
Udzaona zabwino
Nimaona mwa iwe.
Khala bwenzi langa.”
2. Nikada nkhawa,
Pamene mtima wanga univutitsa,
Zimakhala zovuta.
Nimapemphela kwa M’lungu.
Yehova amanimvela.
Nidziŵa anikonda:
(KOLASI)
“Uniyandikile, inenso
N’dzakuyandikila.
Udzaona zabwino
Nimaona mwa iwe.
Khala bwenzi langa.”
(BILIJI)
N’sanam’dziŵe n’dzina lomwe
Anali kun’dziŵa.
Lomba alidi pafupi,
Inde, nthawi zonse.
(KOLASI)
“Uniyandikile, inenso
N’dzakuyandikila.
Udzaona zabwino
Nimaona mwa iwe.
Khala bwenzi langa.”