Yembekeza, Usankhe Bwino
Daunilodi:
1.Nthawi zina nimadzifunsa
N’kwatile ndani?
Komabe ine sinifuna kuthamangila
Sinifuna nikavutike
Mu moyo wanga
Cifukwa zoganiza za ‘cinyamata
Zimasinthasintha.
(KOLASI)
Dekhabe Usathamange
Yembekeza
Ganiza kuti usankhe bwino
Munthu wokuyenelela
Zoona usathamangile
Usathamange
Sankha bwino
2.Ninali kufuna ‘nganisamale
Komanso wonikonda
Komabe sanali kutumikila Yehova
Nifuna kumveladi Yehova pa zinthu zonse
Nidzayembekeza mpaka nipeze
wokondadi Yehova
(KOLASI)
Dekhabe usathamange dekha mtima
Ganiza kuti usankhe bwino
Munthu woyeneleladi
Zoona usathamangile
Usathamangile
Sankha bwino
Sankha bwino