Onani zimene zilipo

Kukaona Malo pa Beteli

Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.

Kuyambilanso Kukayendela Maofesi a Nthambi: Pa June 1, 2023, m'maiko ambili tinayambilanso kulola anthu kukayendela maofesi athu a nthambi. Kuti mumve zambili, funsilani ku ofesi ya nthambi imene mufuna kukayendela. Koma conde, osapitako ngati munapezeka na COVID-19, ngati muli na cimfine, kapena ngati caposacedwa munakhalako pafupi na munthu wodwala COVID-19.

Kazakhstan

Religious Center of Jehovah’s Witnesses in the Republic of Kazakhstan

187 Auezov Street,

Kalkaman-2 micro-district,

ALMATY,

KAZAKHSTAN

+7 727-232-36-62

+7 727-226-30-42

+7 777-223-19-89 (Mobile)

Kuona Malo

Pa Mande mpaka pa Cisanu

8:00hrs mpaka 11:00 hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.

Nthawi yoona malo: Ola limodzi ndi hafu

Zimene Timacita

Timamasulila mabuku ofotokoza Baibulo m’Cikazaki (ca Cisililiki), Cikazaki (ca Ciarabu) ndi Ciwiga (ca Cisililiki).

Tengani kapepala koonetsa malo.